top of page
Search

Utumiki wa abambo pa parishi ya Maula upitilira kulimbikitsidwa

Nthawi ndi nthawi mabungwe komanso miphakati imene ili pansi pa parish ya Maula mu Arkidayosizi ya Lilongwe imatenga nawo gawo pa kutsogolera chipembedzo.


Limodzi mwa mabungwe lomwe layendetsa kale chipembedzo ndi bungwe la a bambo a chiKatolika la CMA ndipo parishi ya Maulayi yathokoza bungweli kamba kodzipereka kwake potsogolera chipembedzo.



Mwazina, abambowo, Loweruka pa 2 May 2026, anakoza mu tchalitchi cha Maula komanso kusamala malo ena pa parishiyi.


Ndipo iwo sanalekere pomwepo ayi, tsiku la Mulungu pa 3 May 2026, anaperekera mphatso za paguwa komaso kuwerenga mau.



Chakumadzulo, abambowa anakumana pamodzi kunyumba ya ansembe a pa parishiyi, pofuna kucheza ngati banja limodzi la pa Maula Cathedral Parishi.



 
 
 

Comments


ABOUT US

We are simply known as a Cathedral of Lilongwe, which is the Capital City of Malawi. We belong to the metropolitan Archdiocese of Lilongwe whose safragan dioceses are Dedza, Mzuzu and Karonga. We follow the Roman or Latin rite.

ADDRESS

+265 (0) 1 755 846

+265 (0) 998 73 35 93

P.O Box 1524, Lilongwe.

parishpriest@maulaparish.org

administration@maulaparish.org

SUBSCRIBE FOR EMAILS

Thanks for submitting!

  • Facebook
  • Instagram
  • Twitter

© 2025 by Team iWork. Proudly created with Wix.com

bottom of page