top of page


"Ukaristiya Thupi ndi Magazi a Ambuye yesu"
Akhristu kuchokera pa parishi ya Maula alangizidwa kukhala anthu okonda kulandira Ukaristia nthawi zonse. Bambo Peter Makina ndi omwe alankhula izi kudzera mu ulaliki wawo pa mwambo wa nsembe ya Misa ya Chaka Cha Ukaristia. Bambo Makina anati akhristu akalandira thupi la Ambuye Yesu moyo wawo udzisinthika popeza "Ukaristia azifanafana ndi Yesu mwini popeza munthu aliyense amakhala chomwe amadya." Ndipo iwo anaonjezera kuti akhristu asanalandire ukaristia, akuyenera kuyamba
Communications
6 days ago1 min read


Parishioners at Maula Cathedral Gather for Corpus Christi Reflection on Eucharistic Adoration
Parishioners of Our Lady of Africa Maula Cathedral came together in a spirit of prayer and deep reflection as they observed the solemnity of Corpus Christi through a special teaching session led by Father Enoch Kanjira, Rector of Kachebere Seminary of Philosophy on June 04th 2026. The gathering, marked by reverence and attentive listening, focused on a deeper understanding of Eucharistic adoration—an essential practice in the Catholic faith that invites believers into a close
Communications
Jun 43 min read


Maula Parish Hosts 'Global Rosary for Peace' Event
The Our Lady of Africa Cathedral (Maula Parish) of the Catholic Archdiocese of Lilongwe has conducted a Global Rosary for Peace event on Saturday, 30th May 2026, at the Maula Parish Grotto. Here is the video of the event by Radio Alinafe. The event aimed to connect local parishioners with Pope Leo XIV and Catholics around the world in Praying The Holy Rosary For Global Peace. To accompany his constant calls for peace in the world, Pope Leo XIV led the prayer of the Holy Rosa
Communications
May 311 min read
Maula Parish to Host 'Global Rosary for Peace' this Saturday
The Maula Parish (Our Lady of Africa) of the Catholic Archdiocese of Lilongwe, has invited the faithful to join a global prayer movement this coming weekend. The parish will host a Global Rosary for Peace event on Saturday, 30th May 2026, starting at 7:00 PM. The evemt will take place at the Maula Parish Grotto. The event aims to unite local parishioners with Pope Leo XIV and Catholics worldwide. Together, we will pray for peace, reconciliation, and hope through the intercess
Communications
May 291 min read


Zochitika pa Tsiku la Chikuku 07 June 2026 ku Parishi ya Maula
(Chithunzi: Ambuye George Tambala pamwambo wakupembedza Ambuye Yesu okhala mu Ukaristia ku Maula Cathedral) Pa 7th June ndi Tsiku la Chikuku, Patsikuli Misa zidzakhala monga mwa nthawi zonse kupatula Misa ya Chilatini yomwe siidzakhalapo. Misa ya Chilatini idzakhalapo pa 14th June 2026. Misa yathu ya Chichewa idzakhalira ku Podium nthawi ya 10 koloko yomwe idzatsogozane ndi Mwambo woyenda ndi Chikuku. Ndipo tidzamalizira ndi Udalitso. Pachifukwa ichi Miphakati ikupemphedwa
Communications
May 251 min read


MAULA CATHEDRAL 2026 MCCB LIST
The Parish would like to congratulate our boys and girls who wrote the MCCB Mock Examination and have passed. The entrance examinations for secondary schools will take place on 20th June 2026 at St. Padre Pio Secondary School in Area 49. ITEMS TO BRING: BUKU LA BANJA LATHU / BAPTISM CARD MANEB ID ITEMS FOR WRITING NO CANDIDATE NAME SEX SMALL CHRISTIAN COMMUNITY CONTACTS BAPT. NO MANEB ID 1 CHIGAMANE Avemaria F St. John Paul II 0881122598 / 0999667708 34/14 2 KWACHA Patience W
Communications
May 201 min read


Maula Cathedral Hosts WUCWO Prayers for Maula Deanery
Catholic women from across Maula Deanery gathered in large numbers at Maula Cathedral on Saturday, 16th May 2026, to celebrate the World Union of Catholic Women’s Organizations (WUCWO) Day of Prayer. The event focused on promoting inner peace, unity, and the critical role mothers play in shaping the future of the Church and the nation. The colorful Eucharistic celebration was led by the Maula Deanery Catholic Women Association (CWA) Chaplain, Rev. Fr. Henderson Kumbasa, and c
Communications
May 162 min read


Chaka chokondwera nkhonswe ya dinale ya Maula mu Arkidayosizi ya Lilongwe mchaka cha 2026
Loweruka pa 2 May 2026, akhristu ochokera m'ma parishi omwe ali pansi pa dinale ya Maula, mu Arkidayosizi ya Lilongwe anasonkhana ku parishi ya St. Denis Ssebuggwawo (Chinsapo) komwe kunachita chaka chokondwerero nkhoswe ya dinale yawo "Amai Maria, Amayi a ku Africa (Our Lady of Africa)." Dinale ya Maula ili ndi ma Parish asanu ndi awiri omwe ndi kuphatikizapo Maula Cathedral, St. Denis Ssebuggwawo (Chinsapo), St. Kizito (Chigoneka), St. Padre Pio (New Gulliver), Maria Mtha
Edwin Sitima
May 31 min read


Utumiki wa abambo pa parishi ya Maula upitilira kulimbikitsidwa
Nthawi ndi nthawi mabungwe komanso miphakati imene ili pansi pa parish ya Maula mu Arkidayosizi ya Lilongwe imatenga nawo gawo pa kutsogolera chipembedzo. Limodzi mwa mabungwe lomwe layendetsa kale chipembedzo ndi bungwe la a bambo a chiKatolika la CMA ndipo parishi ya Maulayi yathokoza bungweli kamba kodzipereka kwake potsogolera chipembedzo. Mwazina, abambowo, Loweruka pa 2 May 2026, anakoza mu tchalitchi cha Maula komanso kusamala malo ena pa parishiyi. Ndipo iwo sanaleke
Edwin Sitima
May 31 min read


Lamulungu La Mayitanidwe ku Parishi ya Maula m'chaka cha 2026
Achinyamata awapempha kumvetsera ndi kuyankha mayitanidwe awo moyenera omwe Mulungu akuwayitanira. Bambo Peter Makina ndi omwe ayankhula izi pa mwambo wa nsembe ya Ukaristiya ya chaka cha mayitanidwe, ku Maula Cathedral mu Arkidayosizi ya Lilongwe. Bambo Makina Bambo Makina anati makolo ali ndi ntchito yambiri yothandiza ndi kulimbikitsa achinyamata kut ayankhe mayitanidwe oyenera, monga moyo wa unsembe, ubulazala, uSisteri komaso moyo wa m'banja, komaso moyo okhala pa yekha.
Edwin Sitima
Apr 291 min read


Lilongwe Women Join Hands in Prayer at Maula Cathedral Grounds: Minister Navicha Pledges Support for Women’s Rights
Women from various Christian denominations gathered at the Maula Cathedral of the Catholic Archdiocese of Lilongwe today, 25th April 2026, to celebrate the World Day of Prayer. This year’s theme, "I Will Give You Rest, Come," was taken from Matthew 11:28-30 and was prepared by the World Day of Prayer Committee of Nigeria. The Guest of Honor, Minister of Gender, Children, Disability and Social Welfare, Honorable Mary Navicha, addressed the gathering with a powerful message. Sh
Communications
Apr 252 min read


Maula Cathedral Hosts Historic Launch of Radio Alinafe Silver Jubilee: A Call to "Invite Christ into Our Challenges"
The church benches of the Maula Cathedral were filled with a spirit of gratitude and anticipation on Sunday, 19th April 2026, as the Catholic Archdiocese of Lilongwe officially launched the Silver Jubilee preparations of Radio Alinafe, marking the beginning of a year-long journey toward April 2027, celebrating the station’s legacy since its founding in 2002. The event, which drew together Catholic journalists, Radio Alinafe volunteers, and hundreds of parishioners, was presid
Communications
Apr 203 min read


La Mulungu La Chifundo cha Mulungu ku Maula Cathedral
Bungwe la Chifundo cha Mulungu pa parishi ya Maula lachita nawo chaka cha la Mulungu la Chifundo cha Mulungu lero pa 12 April 2026. Mwambo wa nsembe ya chakachi unatsogoleredwa ndi bambo Peter Makina. Mu ulariki wawo, bambo Makina anapempha akhristu kukhala okonda kuthandizana nthawi zonse kuphatikizapo pa mavuto osiyanasiyana ndipo kuti adzichita izi ndi chikhulupiliro. Bambo Makina kutsogolera mwambo wa nsembe ya Misa ya Lamulungu la Chifundo cha Mulungu "Tiyeni akhristu t
Communications
Apr 121 min read


ULARIKI WA PA 05 APRIL 2026, LAMULUNGU LA CHAKA CHA PASAKA
Abale ndi alongo okondedwa, Lero tikuyima pano ndi uthenga umodzi wokha, koma waukulu kuposa zonse: Khristu wauka! Inde, wauka ndithu! Aleluya! Mu Uthenga Wabwino wa lero, Yohane akufotokoza za Mariya wa Magadala amene anapita ku manda m'mawa kwambiri. Atafika, anaona mwala wachotsedwa. Ndipo anathamanga kukamuuza Simon Petro NDI wophunzira uja amene Yesu ankankonda kwambiri. Ndipo ones awiri anathamanga, koma wophunzira wina uja anathamanga kuposa Petro. Atafika kumanda Anao
Communications
Apr 53 min read


ZOCHITIKA PA LOWERUKA LOYERA KU MAULA PARISHI MCHAKA CHA 2026
Tsiku la loweruka loyera ndi tsiku lomwe akhristu a mpingo waKatolika amakumbukira kuuka Kwa ambuye Yesu pa dziko lonse lapansi. Parishi ya Amai a ku Afrika - Maula mu Arkidayosizi ya Lilongwe, inachitanso chimodzimodzi motsogozedwa ndi abambo Peter Makina, mwambo omwe unayamba ndi kuyatsa komanso kudalitsa moto, ndipo unakapitira mu tchalitchi cha Maula ndi kuyatsa makandulo. Mu ulaliki wawo, bambo Makina anatsindika kuti monga khristu wauka wakufa, ifenso omutsata tikuyener
Edwin Sitima
Apr 41 min read


Good Friday Reflection: The Passion of the Lord at Maula Cathedral
Following the Way of the Cross, the community at Maula Cathedral gathered for the Passion of the Lord , led by Father Peter Makina. The liturgy was marked by a profound moment of silence and symbolism known as the Prostratio . The Meaning of the Prostratio At the beginning of the Good Friday liturgy, the priest lies face down before the altar in absolute silence. This "total surrender" is a physical prayer that speaks where words fall short. Aspect What it Expresses Humility
Communications
Apr 31 min read


Solemn Way of the Cross Held at Our Lady of Africa - Maula Cathedral
Catholic faithful at Our Lady of Africa Maula Cathedral, led by Father Peter Makina, took part in the solemn spiritual journey of the Stations of the Cross on Good Friday this year. The Way of the Cross commenced from Maula Parish gate; Proceeding along M1 road; Turning into Paul Kagame Road; Passing by Amina House; Continuing through Area 6 up to Crossroads and then concluding at the Cathedral. Vice President Dr. Jane Ansah joined the procession, highlighting the importance
Communications
Apr 31 min read


Catholic Archdiocese of Lilongwe Holds Chrism Mass at Maula Cathedral
On Tuesday, 31 March 2026, the Catholic Archdiocese of Lilongwe held a Chrism Mass at Maula Cathedral, bringing together priests, religious, and lay faithful from across the archdiocese. The Mass was presided over by the Auxiliary Bishop of Lilongwe Archdiocese, His Lordship Bishop Vincent Fredrick Mwakhwawa, DP, marking his first-ever Chrism Mass celebration since his episcopal ordination in January 2024. During the liturgy, Bishop Mwakhwawa blessed the Holy Oils and led the
Communications
Mar 313 min read


ANA A TILITONSE OCHOKERA KU MAULA PARISH ACHITA NTCHITO ZA CHIFUNDO PA NDENDE YA MAULA (LILONGWE)
Loweruka pa 28 March 2026, ana a Tilitonse ochokera pa parishi ya Maula apereka thandizo la zinthu zosiyanasiyana pa ndende ya Maula mu mzinda wa Lilongwe. Anawa akwanitsa kuYendera ana anzawo omwe ali mndende ngati njira imodzi yochita za chifundo mu nyengo ino ya lenti. M’mawu awo, ena mwa ana a Tilitonse ochokera pa parishiyI, Stephano Mavuto komanso Giniya Sibino ati kupita ku ndende ya Maula kwakhala kowathandiza kugawana ndi anzawo za maphunziro omwe amaphunzira ku tch
Communications
Mar 282 min read


Maula Cathedral Legionaries Celebrate the Solemnity of the Annunciation at St. Anthony of Padua’s Parish
On March 25, 2026, the Catholic Church worldwide celebrated the Solemnity of the Annunciation of the Lord, commemorating the moment the Angel Gabriel announced to the Virgin Mary that she would conceive Jesus through the power of the Holy Spirit. Occurring exactly nine months before Christmas, this feast highlights the mystery of the Incarnation and Mary’s profound “yes” to God’s will. In the Archdiocese of Lilongwe, the day held special significance for the Legionaries of Ma
Edwin Sitima
Mar 261 min read
bottom of page