top of page
Edwin Sitima
Writer
Contributor
More actions
Profile
Join date: Oct 7, 2025
Posts (24)
Jun 13, 2026 ∙ 1 min
Sukulu ya Mlale Minor Seminale iyendera Parish ya Maula
Ophunzira ochokera ku sukulu ya St. Paul Minor Seminary - Mlale mu Arkidayosozi ino ya Lilongwe alimbikitsidwa kukhala okonda maphunziro awo. Izi zayankhulidwa ndi a Chapola, omwe ndi wapampando wa akhristu omwe amapephera Misa ya Latin ku Maula Cathedral. A Chapola ati ali ndi chiyembekezo kut ena mwa anyamatawa adzakhala ansembe, poti munda wakula achepa ndi ntchito. "Inu achinyamata limbikirani maphunziro anu kut ena mwa inu mudzatumikire Mulungu. Ndipo bambo Peter Makina anathokoza...
3
0
May 3, 2026 ∙ 1 min
Chaka chokondwera nkhonswe ya dinale ya Maula mu Arkidayosizi ya Lilongwe mchaka cha 2026
Loweruka pa 2 May 2026, akhristu ochokera m'ma parishi omwe ali pansi pa dinale ya Maula, mu Arkidayosizi ya Lilongwe anasonkhana ku parishi ya St. Denis Ssebuggwawo (Chinsapo) komwe kunachita chaka chokondwerero nkhoswe ya dinale yawo "Amai Maria, Amayi a ku Africa (Our Lady of Africa)." Dinale ya Maula ili ndi ma Parish asanu ndi awiri omwe ndi kuphatikizapo Maula Cathedral, St. Denis Ssebuggwawo (Chinsapo), St. Kizito (Chigoneka), St. Padre Pio (New Gulliver), Maria Mthandizi wa Akhristu...
10
0
May 3, 2026 ∙ 1 min
Utumiki wa abambo pa parishi ya Maula upitilira kulimbikitsidwa
Nthawi ndi nthawi mabungwe komanso miphakati imene ili pansi pa parish ya Maula mu Arkidayosizi ya Lilongwe imatenga nawo gawo pa kutsogolera chipembedzo. Limodzi mwa mabungwe lomwe layendetsa kale chipembedzo ndi bungwe la a bambo a chiKatolika la CMA ndipo parishi ya Maulayi yathokoza bungweli kamba kodzipereka kwake potsogolera chipembedzo. Mwazina, abambowo, Loweruka pa 2 May 2026, anakoza mu tchalitchi cha Maula komanso kusamala malo ena pa parishiyi. Ndipo iwo sanalekere pomwepo ayi,...
28
0
bottom of page